Letras
nkazi ine mutu zwee, iwe olo ntima kugunda?
koma ndingakozedwe ima kaye ndingotunda iweyo uli on fire koma sukuyaka ngati mafuwa umapangisa mdima masana ndiwe chiphadzuwa, tadikila pang'ono ndufuna ntakamba nawe